Трек очень похож на
- Название Umpeze Wina
- Исполнитель Maskal
- Жанр R&B/Soul
Видео
Текст песни
Wakhala ukundinamiza
Ndinakupasa mwayi omaliza
Lero wapanganso chimodzimodzi ndatopandatopa
Iwe munthu wantundu wanji
Kunamiza munthu umamva bwanji
Ndinayesa kupeleka chikondi ndatopandatopa
Chikondi chomwe mnapeleka kwa iwe
Ndichomwe chinatsala mtima mwa ine
Sindingakwanitse kukhala ndi iwe
Ndapita! Ndapita

